Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Kodi Mungatani Kuti Mulungu Azikukondani?
Photo Credits:
■ Page 16: Buena Vista Images
■ Page 161: Mixa/age fotostock
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka ndalama, pitani pa webusaiti yathu ya jw.org/ny.
Malemba onse m’bukuli achokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Losindikizidwa mu February 2018
Chichewa (lvs-CN)
© 2017
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania