Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Kuphunzira Malemba Tsiku ndi Tsiku—2020
Lemba la Chaka “Pitani mukaphunzitse anthu . . . kuti akhale ophunzira anga. Muziwabatiza.”—Mateyu 28:19.
Kabukuka sitigulitsa. Timakapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’kabukuka akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Kosindikizidwa mu June 2019
Chichewa (es20-CN)
© 2019
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA