Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
MLUNGU WA APRIL 2-8, 2018
3 Tizikhala Okhulupirika Komanso Omvera Ngati Nowa, Danieli ndi Yobu
MLUNGU WA APRIL 9-15, 2018
8 Kodi Mumadziwa Yehova Ngati Mmene Nowa, Danieli ndi Yobu Ankamudziwira?
Nowa, Danieli ndi Yobu anakumana ndi mavuto ofanana ndi amene timakumana nawo masiku ano. Kodi n’chiyani chinawathandiza kudziwa bwino Yehova? Nanga n’chiyani chinawathandiza kuti akhalebe okhulupirika ndiponso omvera? Nkhani ziwirizi ziyankha mafunso amenewa.
MLUNGU WA APRIL 16-22, 2018
18 Kodi Kukhala Munthu Wauzimu Kumatanthauza Chiyani?
MLUNGU WA APRIL 23-29, 2018
Nkhani yoyamba ikufotokoza tanthauzo la munthu wauzimu komanso zimene tingaphunzire kwa anthu amene anasonyeza kuti ndi auzimu. Nkhani yachiwiri ikufotokoza zimene tingachite kuti tizikula mwauzimu komanso mmene kukhala munthu wauzimu kungatithandizire pa moyo wathu.