December 3-9
MACHITIDWE 9-11
Nyimbo Na. 115 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Munthu Amene Ankazunza Akhristu Anakhala Mkhristu Wakhama”: (10 min.)
Mac. 9:1, 2—Saulo ankazunza kwambiri ophunzira a Yesu (bt 60 ¶1-2)
Mac. 9:15, 16—Saulo anasankhidwa kuti azichitira umboni za Yesu (w16.06 7 ¶4)
Mac. 9:20-22—Saulo anakhala Mkhristu wakhama (bt 64 ¶15)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Mac. 9:4—N’chifukwa chiyani Yesu anafunsa Saulo kuti: “N’chifukwa chiyani ukundizunza?” (bt 60-61 ¶5-6)
Mac. 10:6—N’chifukwa chiyani n’zochititsa chidwi kuti mtumwi Petulo ankakhala kunyumba kwa munthu wofufuta zikopa? (“Simoni, wofufuta zikopa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mac. 10:6, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mac. 9:10-22
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl mutu 6
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (8 min.)
Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 16
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero