Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb19.06 3
  • June 10-16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 10-16
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19.06 3

June 10-16

AEFESO 1-3

  • Nyimbo Na. 112 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Ulamuliro wa Yehova Ukuchita”: (10 min.)

    • [Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Aefeso.]

    • Aef. 1:8, 9​—“Chinsinsi chopatulika” ndi chokhudza Ufumu wa Mesiya (it-2 837 ¶4)

    • Aef. 1:10​—Yehova akugwirizanitsa anthu komanso angelo (w12 7/15 27-28 ¶3-4)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Aef. 3:13​—Kodi masautso a Paulo ‘ankatanthauza ulemerero’ kwa Aefeso m’njira yotani? (w13 2/15 28 ¶15)

    • Aef. 3:19​—Kodi timadziwa bwanji “chikondi cha Khristu”? (cl 299 ¶21)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aef. 1:1-7 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 3)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musonyezeni chimodzi mwa zinthu zimene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu. (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 95

  • “Muzipindula Mokwanira Mukamaphunzira Panokha”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Pitirizani “Kugwira Mwamphamvu Mawu a Moyo” Pophunzira Mwakhama.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs 6:1-7

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 46 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani