Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.03 4
  • March 8-14

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 8-14
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.03 4

March 8-14

NUMERI 9–10

  • Nyimbo Na. 31 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amatsogolera Anthu Ake”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 9:13​—Kodi tikuphunzira chiyani pa malangizo amene Aisiraeli anapatsidwawa? (it-1 199 ¶3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 10:17-28 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene poitanira anthu ku Chikumbutso. Pambuyo poti mwininyumba wasonyeza chidwi, yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Tizikumbukira Imfa ya Yesu kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 11)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Itanirani ku Chikumbutso mnzanu wakuntchito kapena wakusukulu amene munamulalikirapo m’mbuyomu. (th phunziro 2)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) bhs 5:Bokosi. Muitanireni ku Chikumbutso ndipo mufotokozereni kuchokera m’Baibulo chifukwa chake sayenera kukadya zizindikiro. (th phunziro 17)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 84

  • Kusintha Zinthu pa Beteli Kukuthandiza pa Ntchito Yolalikira: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi pamsonkhano wapachaka wa 2015 panaperekedwa chilengezo chotani, nanga ndi zifukwa ziwiri ziti zomwe zinachititsa kuti pakhale kusintha? Kodi ndi zinthu zina ziti zimene zinasintha pa Beteli, ndipo kusinthaku kwathandiza bwanji? Kodi chilengezochi chinakhudza bwanji ntchito yosamutsa nthambi ya ku Britain? Kodi kusintha kumeneku kukusonyeza bwanji kuti Yehova akutitsogolera?

  • Chimene Tinabwerera ku Beteli: (5 min.) Onerani vidiyoyi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia 17:9-17

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani