Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb21.03 9
  • March 22-28

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 22-28
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21.03 9

March 22-28

NUMERI 13-14

  • Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mmene Chikhulupiriro Chimatithandizira Kukhala Olimba Mtima”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 13:27​—Kodi ndi zinthu ziti zimene azondi ananena zomwe zikanathandiza Aisiraeli kukhulupirira kwambiri Yehova? (Le 20:24; it-1 740)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 13:1-16 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Nkhani: (5 min.) w15 9/15 14-16 ¶8-12​—Mutu: Mafunso Amene Angatithandize Kudziwa Mmene Chikhulupiriro Chathu Chilili. (th phunziro 14)

  • “Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki​—Muzifunsa Mafunso”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa​—Muzifunsa Mafunso.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 73

  • N’chifukwa Chiyani Akhristu Oona Amafunika Kulimba Mtima?​—Kuti Azilalikira: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi Kitty Kelly anakumana ndi vuto lotani? N’chiyani chinamuthandiza kuti ayambe kuchita zinthu molimba mtima? Nanga anapeza madalitso otani?

  • N’chifukwa Chiyani Akhristu Oona Amafunika Kulimba Mtima?​—Kuti Asamalowerere Ndale: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi Ayenge Nsilu ankakumana ndi mavuto otani? Kodi n’chiyani chinamuthandiza kuti apitirizebe kuchita zinthu molimba mtima? Nanga kodi anamvetsa mfundo iti imene inamuthandiza kuti azidalira Yehova?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia 18:1-8

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 15 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani