Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.09 24
  • Kufikira Pamene Adzakhalenso Ndi Moyo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kufikira Pamene Adzakhalenso Ndi Moyo
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Mungachite Mukaferedwa
    Nkhani Zina
  • Yesu Ali ndi Mphamvu Zoukitsa Anthu Amene Anamwalira
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Timakhulupirira Kuti Anthu Amene Anamwalira Adzauka
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2020
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.09 24
Mayi wakumbatira mwana wake amene waukitsidwa m’Paradaiso.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kufikira Pamene Adzakhalenso Ndi Moyo

Munthu amene timam’konda akamwalira timatonthozedwa tikaganizira kuti adzaukitsidwa. Ngakhale zili choncho, uchimo komanso imfa zili ngati chophimba chimene chimatiphimba tonsefe ndipo chimatisowetsa mtendere. (Yes 25:7, 8) N’chifukwa chake “chilengedwe chonse chikubuula limodzi ndi kumva zowawa.” (Aro 8:22) Kodi tingatani kuti tipirire imfa ya okondedwa athu kufikira pamene adzakhalenso ndi moyo? M’Mawu a Mulungu muli mfundo zimene zingatithandize.

ONERANI VIDIYO YAKUTI ZIMENE MUNGACHITE MUKAFEREDWA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi Danielle komanso Masahiro ndi Yoshimi anakumana ndi mavuto otani?

  • Kodi mfundo 5 zotchulidwa mu vidiyoyi zinawathandiza bwanji?

  • Kodi ndi ndani amene amatitonthoza?​—2Ak 1:3, 4

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani