Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb22.11 10
  • November 28–December 4

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 28–December 4
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22.11 10

November 28-December 4

2 MAFUMU 11-12

  • Nyimbo Na. 59 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mzimayi Woipa Komanso Wodzimva Analangidwa”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 12:1​—N’chifukwa chiyani Yehova sanalole kuti Yehoasi aphedwe ali mwana? (it-1 1265-1266)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 11:1-8 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Muitanireni ku misonkhano yathu, ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu kwaulere ndipo mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 3)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 08 mawu oyamba a pa Fufuzani Mozama ndi mfundo 4 (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 84

  • “N’chifukwa Chiyani Akhristu Akufunika Kuyesetsa Kuti Akhale Ndi Zolinga?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Mukufunika Kuyesetsa Kuti Mukhale Woyang’anira? (1Ti 3:1)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 19, Mfundo 1-4

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani