Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.01 15
  • February 6-12

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 6-12
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.01 15

February 6-12

1 MBIRI 10-12

  • Nyimbo Na. 94 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzikhala Wofunitsitsa Kuchita Zimene Mulungu Amafuna”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Mb 12:33​—Kodi amuna 50,000 a fuko la Zebuloni anapereka bwanji chitsanzo chabwino? it-1 1058:5-6)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mb 11:26-47 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 6)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 09 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 18)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 97

  • “Muzidziwa Mmene Yehova Amaganizira”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • “Khalani ndi Zolinga pa Nyengo ya Chikumbutso”: (5 min.) Nkhani yokambirana.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 28

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 19 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani