Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.09 2
  • September 4-10

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • September 4-10
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.09 2

September 4-10

ESITERE 1-2

  • Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesetsani Kukhala Odzichepetsa Ngati Esitere”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Est 2:5—Kodi pali umboni wotani umene umatsimikizira kuti nkhani ya m’Baibulo ya Moredekai ndi yoona? (w22.11-CN 31:3-6)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Est 1:​13-20 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Ufumu—Mt 6:​9, 10. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni kabuku kakuti, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 1)

  • Nkhani: (5 min.) w20.11 12-14 ¶3-7—Mutu: Anathandizidwa ndi Yesu Komanso Angelo. (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 106

  • Zimene Achinyamata Anzanu Amanena—Maonekedwe: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: N’chifukwa chiyani nthawi zina zingakhale zovuta kukhala ndi maganizo oyenera pa nkhani ya mmene timaonekera?

    Kodi mfundo ya pa lemba la 1 Petulo 3:​3, 4 ingatithandize bwanji kukhala ndi maganizo oyenera pa nkhani ya mmene timaonekera?

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 49:1-5

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani