CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Anagwiritsa Ntchito Udindo Wake Pothandiza Anthu Ena
Moredekai anapatsidwa udindo waukulu kwambiri (Est 9:4; it-2 432:2)
Iye anayambitsa chikondwerero cha chaka ndi chaka pofuna kulemekeza Yehova (Est 9:20-22, 26-28; it-2 716:5)
Iye ankachitira zabwino anthu a Mulungu (Est 10:3)
Masiku ano, anthu amene ali ndi udindo m’gulu la Yehova amayesetsa kutsanzira chitsanzo cha Moredekai.—cl-CN 101-102:12-13.