Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb23.09 12
  • October 2-8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 2-8
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23.09 12

October 2-8

YOBU 1-3

  • Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yob 1:10—Kodi lembali likutithandiza bwanji kumvetsa mawu a Yesu opezeka pa lemba la Mateyu 27:46? (w21.04 15:9)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 3:​1-15 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 9)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo?, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 20)

  • Nkhani: (5 min.) w22.01 2:11-14—Mutu: Tiziphunzitsa Mogwira Mtima Ngati Yakobo—Tizipereka Malangizo Mosapita M’mbali Komanso Tizikhala Odzichepetsa. (th phunziro 18)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 21

  • Ndinkaganiza Ngati Ndili Ndi Chilichonse: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: N’chifukwa chiyani M’bale Birdwell ankaganiza kuti anali ndi chilichonse?

    Kodi kuganizira mfundo ya pa lemba la Mateyu 6:33 kunathandiza bwanji m’baleyu?

    Kodi mwaphunzirapo chiyani pa chitsanzo cha banja la a Birdwell?

  • “Muzigwiritsa Ntchito Tsamba Loyamba la JW.ORG Mukakhala mu Utumiki”: (5 min.) Nkhani yokambirana.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 51

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani