Magazini Yophunzira
JANUARY 2020
NKHANI ZOPHUNZIRA: MARCH 2–APRIL 5, 2020
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
LEMBA LA CHAKA CHA 2020:
“Pitani mukaphunzitse anthu . . . kuti akhale ophunzira anga. Muziwabatiza.”—MAT. 28:19.
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Yesu ataukitsidwa anakumana ndi atumwi komanso anthu ena ku Galileya ndipo anawauza kuti “pitani mukaphunzitse anthu . . . kuti akhale ophunzira anga” (Onani nkhani yophunzira 1, ndime 3-4)