Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • w21.10
  • Magazini Yophunzira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Magazini Yophunzira
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
w21.10
Nsanja ya Olonda Yophunzira, October 2021.

Magazini Yophunzira

OCTOBER 2021

NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: DECEMBER 6, 2021–JANUARY 2, 2022

© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.

Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:

Ngakhale kuti Nowa analalikira mokhulupirika kwa zaka zambiri, palibe amene analowa m’chingalawa kupatulapo iye ndi anthu a m’banja lake. Ngakhale zinali choncho, Nowa ankamverabe Mulungu. (Onani nkhani yophunzira 43, ndime 11)

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani