Mawu a M'munsi
b Yehova ankalandira nsembe zanyama zimene anthu okhulupirika omwe anakhalapo Chikhristu chisanayambe ankapereka, chifukwa ankadziwa kuti m’tsogolo Yesu Khristu adzapereka moyo wake kuti apulumutse anthu ku uchimo ndi imfa mpaka kalekale.—Aroma 3:25.