-
Yohane 4:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Munthuyu atamva kuti Yesu wafika ku Galileya kuchokera ku Yudeya, anapita kwa iye ndi kuyamba kumupempha kuti apiteko ndi kukachiritsa mwana wakeyo, pakuti anali pafupi kumwalira.
-