LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
Baibo ya Cimasulilo ca Dziko Latsopano

Za m’Buku la Agalatiya

AGALATIYA

ZA M’BUKULI

  • 1

    • Moni (1-5)

    • Palibe uthenga wina wabwino (6-9)

    • Uthenga wabwino umene Paulo analalikila ndi wocokela kwa Mulungu (10-12)

    • Kutembenuka kwa Paulo komanso nchito zake zoyambilila (13-24)

  • 2

    • Paulo akumana ndi atumwi ku Yerusalemu (1-10)

    • Paulo adzudzula Petulo (Kefa) (11-14)

    • Munthu amaonedwa wolungama cifukwaca cikhulupililo (15-21)

  • 3

    • Nchito za Cilamulo komanso cikhulupililo (1-14)

      • Wolungama adzakhala ndi moyo cifukwa ca cikhulupililo (11)

    • Lonjezo la Abulahamu silidalila Cilamulo (15-18)

      • Khristu, mbadwa ya Abulahamu (16)

    • Ciyambi ca Cilamulo komanso colinga cake (19-25)

    • Ana a Mulungu cifukwa ca cikhulupililo (26-29)

      • Ake a Khristu ndi mbadwa za Abulahamu (29)

  • 4

    • Sindinunso akapolo koma ana (1-7)

    • Nkhawa ya Paulo kwa Agalatiya (8-20)

    • Hagara ndi Sara: zipangano ziwili (21-31)

      • Yerusalemu wokwezeka ndi mfulu ndipo ndi mai wathu (26)

  • 5

    • Ufulu wa Akhristu (1-15)

    • Kuyenda mwa mzimu (16-26)

      • Nchito za thupi (19-21)

      • Cipatso ca mzimu (22, 23)

  • 6

    • Muzinyamuzana mitolo (1-10)

      • Timakolola zimene tabzyala (7, 8)

    • Kucita mdulidwe kulibe phindu (11-16)

      • Kulengedwa mwatsopano (15)

    • Mau othela (17, 18)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani