LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • g18 na. 2 tsa. 2
  • Mau oyamba

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mau oyamba
  • Galamuka!—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Muyenela Kucita Ciyani Kuti Banja Lanu Likhale Lacimwemwe?—Mbali 2
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Mawu Oyamba
    Galamuka!—2019
Galamuka!—2018
g18 na. 2 tsa. 2

Mau oyamba

Zinsinsi 12 za Mabanja Acimwemwe

Timamva zifukwa zosiyana-siyana zimene zimapangitsa mabanja kupasuka.

  • M’zaka za pakati pa 1990 ndi 2015, ciŵelengelo ca osudzulana ku America cinawonjezeka kuwilikiza kaŵili kwa anthu a zaka zopitilila 50. Ndipo a zaka zopitilila 65 ciŵelengelo cawo cinawilikiza katatu.

  • Akatswili ena amalimbikitsa makolo kuti nthawi zonse aziyamikila ana awo. Enanso amakamba kuti azilanga ana awo mwamphamvu na colinga cofuna kuwathandiza. Conco, makolo sadziŵa zimene angacite.

  • Acicepele amakula, koma osadziŵa maluso ofunikila kuti akhale na umoyo wabwino.

Nanga cimathandiza mabanja ena kukhala acimwemwe n’ciani? Zoona n’zakuti . . .

  • Ukwati ungakhale wokondweletsa komanso mgwilizano wa moyo wonse.

  • Makolo angaphunzile kupeleka cilango mwacikondi kwa ana awo.

  • Acicepele angaphunzile maluso amene angafunikile akadzakula.

Motani? Magazini ino ya Galamuka! idzafotokoza zinsinsi 12 za mabanja acimwemwe.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani