Thandizo Kwa Ofedwa
Na. 3 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Nchitoyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu.Kuti mupeleke copeleka canu, yendani pa webusaiti ya www.jw.org. Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.