Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
Njila ya Kumoyo Wamuyaya—Kodi Mwaipeza?
Buku ili si logulitsa. Colinga cake ni kuthandiza panchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.
Kuti mupange copeleka, pitani pa copeleka.jw.org
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Koma tasintha masipeling’i kuti agwilizane ndi Cinyanja cimene talemba.
Kupulinta kwa mu 2011
Cinyanja (ol-CIN)
© 2002
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania