Cikuto Cakumbuyo
Mungaonetse bwanji kuti mumam’kondadi Mulungu?
Ndi liti pamene muyenela kudalila cikumbumtima canu?
Kodi mabwenzi amene mumasankha amaonetsa ciani za inu?
Kodi mmene mumaonela ulamulilo zimakhudza motani mmene Mulungu amakuonelani?
N’cifukwa ciani mudzapindula ngati mutsatila mfundo za Mulungu za makhalidwe abwino?
Mungacite ciani kuti mupeze cisangalalo pa nchito yanu?
N’ciani cidzakuthandizani kukhala ofunitsitsa kumvela Yehova?