Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu
Kanapulintiwa mu August 2018
Cinyanja (fg-CIN)
© 2012
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA
Kabuku aka si kogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.
Ngati mufuna kupeleka zothandizila pa nchitoyi, yendani pa www.pr2711.com.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, masipeling’i a Cinyanja m’kabuku kano tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages
Photo Credits:
Page 6, top, Dead Sea Scroll: Shrine of the Book, Photo © The Israel Museum, Jerusalem; page 6, middle, and page 32, upper right, Greek Codex: From The Codex Alexandrinus in Reduced Photographic Facsimile, 1909, by permission of the British Library; page 16, Hitler: Based on U.S. National Archives photo