Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
Phunzitsani Ana Anu
© 2014
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Ofalitsa
Watch Tower Bible and Tract Society Of South Africa NPC,1 Robert Broom Drive East, Rangeview, Krugersdorp, 1739, R.S.A.
Kusindikiza kwa mu October 2013
Kabuku aka si kogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibulo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.
Baibulo limene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa lina. Komabe, masipeling’i a Cinyanja m’kabuku kano tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.