Mau Oyamba
Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, ndi mphamvu zako zonse. Mau awa amene ndikukulamula lelo azikhala pamtima pako, ndi kuwakhomeleza mwa ana ako. Uzilankhula nao za mauwo ukakhala pansi m’nyumba mwako, poyenda pamseu, pogona ndi podzuka. —DEUTERONOMO 6:5-7.