Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
Mayankho pa Mafunso 10 Amene Acicepele Amafunsa
Acicepele ena amene tawagwila mau maina awo taasintha.
Kabuku kano si kogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa anthu Baibo pa dziko lonse lapansi. Nchitoyi timaiyendetsa mwa zopeleka zaufulu.
Kuti mutumize copeleka canu, yendani pa www.pr2711.com.
Baibo yamene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina.
Kanapulinthiwa mu May 2016
Cinyanja (ypq-CIN)
© 2016
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania