Zamkati
1 Mulungu Anapanga Kumwamba na Dziko Lapansi
2 Mulungu Anapanga Mwamuna na Mkazi Oyamba
Kucokela pa Adamu Mpaka pa Cigumula ca Nowa
3 Adamu na Hava Sanamvele Mulungu
6 Anthu 8 Anapulumuka na Kuloŵa m’Dziko Latsopano
Kucokela pa Cigumula ca Nowa Mpaka pa Yakobo
8 Abulahamu na Sara Anamvela Mulungu
9 Mpaka Anakhala na Mwana Wake!
13 Yakobo na Esau Akhalanso pa Mtendele
Kucokela pa Yosefe Mpaka pa Kuwoloka Nyanja Yofiila 38
14 Kapolo Amene Anamvela Mulungu
15 Yehova Sanamuiŵalepo Yosefe
17 Mose Anasankha Kulambila Yehova
22 Cozizwitsa pa Nyanja Yofiila
32 Mtsogoleli Watsopano na Azimayi Aŵili Olimba Mtima
34 Gidiyoni Agonjetsa Amidiyani
35 Hana Apemphela Kuti Akhale na Mwana
38 Yehova Anapatsa Samsoni Mphamvu
42 Yonatani, Munthu Wolimba Mtima Komanso Wokhulupilika
Kucokela pa Solomo Mpaka pa Nthawi ya Eliya 106
46 Mulungu Woona Adziŵika pa Phili la Karimeli
48 Mwana wa Mkazi Wamasiye Aukitsidwa
Kucokela pa Elisa Mpaka pa Nthawi ya Yosiya
51 Kamtsikana Kathandiza Mkulu wa Asilikali
53 Yehoyada Anali Wolimba Mtima
54 Yehova Anamulezela Mtima Yona
55 Mngelo wa Yehova Ateteza Hezekiya
56 Yosiya Anali Kukonda Cilamulo ca Mulungu
Kucokela pa Yeremiya Mpaka pa Nthawi ya Nehemiya
57 Yehova Atumiza Yeremiya Kuti Akalalikile
59 Anyamata Anayi Amene Anamvela Yehova
60 Ufumu Umene Udzalamulila Kwamuyaya
62 Ufumu Woimilidwa na Mtengo Waukulu
64 Danieli Anaponyedwa m’Dzenje la Mikango
65 Esitere Apulumutsa Anthu a Mtundu Wake
66 Ezara Aphunzitsa Cilamulo ca Mulungu
67 Mpanda wa Yerusalemu Umangidwanso
69 Gabirieli Aonekela kwa Mariya
70 Angelo Alengeza za Kubadwa kwa Yesu
72 Pamene Yesu Anali Wacicepele
74 Pamene Yesu Anakhala Mesiya
77 Mzimayi Akumana na Yesu pa Citsime
78 Yesu Analalikila Uthenga wa Ufumu
79 Yesu Acita Zozizwitsa Zambili
82 Yesu Anaphunzitsa Otsatila Ake Kupemphela
83 Yesu Adyetsa Khamu la Anthu
Wiki ya Yesu Yothela pa Dziko Lapansi
92 Yesu Aonekela kwa Ophunzila Ake Asodzi
Cikhristu Cifalikila ku Madela Ena
94 Ophunzila a Yesu Alandila Mzimu Woyela
95 Palibe Akanawaletsa Kulalikila
97 Koneliyo Alandila Mzimu Woyela
98 Cikhristu Cifalikila ku Madela Akutali