Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
Citani Khama Pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa—1 Timoteyo 4:13
Kabuku kano si kogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu.
Ngati mufuna kupeleka zothandizila pa nchitoyi, yendani pa www.pr2711.com.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano, kusiyapo ngati taonetsa ina.
Apply Yourself to Reading and Teaching
Kanapulintiwa mu July 2018
Cinyanja (th-CIN)
© 2018
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Ofalitsa