Tsamba la Mutu wa Buku/Tsamba la Ofalitsa
Kondani Anthu Kuti Mupange Ophunzila
Kabuku kano si kogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa mwa zopeleka zaufulu.
Kuti mutumize copeleka canu, pitani pa donate.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.
Love People—Make Disciples
Inapulintidwa mu October 2023
Cinyanja (lmd-CIN)
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania