‘Kulambira Mulungu Motsogoleredwa ndi Mzimu Komanso Coonadi’
M’mawa
8:40 Nyimbo Zamalimba
8:50 Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero
9:00 “Atate Akufuna . . . Anthu Ngati Amenewo”
9:15 Yosiyirana: ‘Muzilambira Mulungu Motsogoleredwa ndi Mzimu’
• Pamene Mufuna Kumvetsetsa Malangizo a Yehova
• Pamene Mukulimbana ndi Zolefula
• Pamene Mukuyesetsa Kucita Zambiri
10:05 Nyimbo Na. 88 ndi Zilengezo
10:15 Mmene Timacititsira Kuti Coonadi ‘Cidziwike’
10:35 Ubatizo: Cifukwa Cake Ubatizo Wanu ndi Wofunika
11:05 Nyimbo Na. 51
Masana
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 72 ndi Pemphero
12:35 Nkhani ya Anthu Onse: Kodi Tingasiyanitse Bwanji Coyenera ndi Cosayenera?
13:05 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:35 Nyimbo Na. 56 ndi Zilengezo
13:45 Yosiyirana: ‘Muzilambila Mulungu Motsogoleredwa ndi. . . Coonadi’
• M’banja
• M’dziko Logawikanali
• Mukamakumana ndi Mabvuto a Zacuma
14:30 “Gula Coonadi Ndipo Usacigulitse”
15:00 Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero