Magazini Yophunzila
JANUARY 2017
NKHANI ZOPHUNZILA: FEBRUARY 27–APRIL 2, 2017
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
CHILE
Ofalitsa a kum’mwela kwa dziko la Chile akuyenda m’mbali mwa mtsinje wodutsa m’nkhalango na m’mapili a Andes okhala ndi sinowu (snow) pamwamba pake. Ali pa nchito yapadela yokalalikila kwa anthu akutali pamene nyengo yakhalako bwino.
OFALITSA
76,296
MAPHUNZILO A BAIBO
64,178
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2015)
174,761
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi ni zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.