Magazini Yophunzila
SEPTEMBER 2017
NKHANI ZOPHUNZILA: OCTOBER 23–NOVEMBER 26, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
EL SALVADOR
Mabanja aŵili akucita ulaliki wapoyela poseŵenzetsa tumashelufu twamawilo. Iwo ali pafupi na imodzi mwa mashopu akulu-akulu ku San Salvador
OFALITSA
41,084
MAPHUNZILO A BAIBO
42,813
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2016)
92,606
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.