Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Mmene Mungathandizile Ana Anu pa Nkhani ya Moŵa
Ni liti pamene mufunika kuyamba kukambilana ndi ana anu zokhudza moŵa? Nanga mungakambilane nawo bwanji?
Pa jw.org, pitani ku Chichewa pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA kenako pa ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA> KULERA ANA.
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Khungu la Nangumi Lotha Kudziyeletsa Lokha
N’cifukwa ciani asayansi afuna kutengela khungu la nangumi lotha kudziyeletsa lokha?
Pa jw.org, pitani ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA kenako pa BAIBULO KOMANSO SAYANSI > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?