Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
Tsanzilani Cikhulupiriro Chawo
Kodi zinatheka bwanji kuti anthu aŵili osiyana kwambili cikhalidwe na msinkhu ayambe kugwilizana kwambili? Kodi citsanzo cawo cingakuthandizeni bwanji kupeza anzanu abwino?
Pa jw.org, pitani ku Chichewa pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUKHULUPIRIRA MULUNGU > TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO.
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Luso la Nyelele Lopukuta Tinyanga Take
Kanyelele kameneka kamafunika kupukuta tunyanga twake kuti kasafe. Kodi kamapukuta bwanji?
Pa jw.org, pitani ku Chichewa pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Pitani pa webusaiti ya jw.org®, kapena unikani kacidindo aka