Zilengezo
◼ Cogaŵila ca mu July ndi August: Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu! kapena kabuku kena kalikonse koonetsedwa pansipa ka masamba 32: Mungathe Kukhala Bwenzi la Mulungu!, Mvetselani kwa Mulungu, ndi Mvetselani kwa Mulungu kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya. September ndi October: Magazini a Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani!
◼ Zofalitsa Zimene Zilipo m’Ciwemba: Buku Langa La Nkhani za m’Baibo, ndi DVD ya Nowa ndi Davide.
◼ Zofalitsa Zimene Zilipo m’Cimambwe-Lungu: Ndani Amene Akucita Cifunilo ca Yehova Masiku Ano?, Mizimu ya Akufa, ndi Njila ya Kumoyo Wamuyaya—Kodi Mwaipeza?
◼ Zofalitsa Zimene Zilipo m’Cinsenga ndi Cilala-Bisa: Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wosatha, ndi Mvetselani kwa Mulungu.
◼ Kodi mungasamuke ndi kuthandiza mipingo iyi imene ili ndi ofalitsa Ufumu ocepa?
Cilozi: Kalwalo; Nakaunga W-01; Ndanda; Nakako W-02; Kasha; Lutwi W-03; Mukwe; Nambungu W-04; Sikachele; Makunka W-05; Ikwe W-06
Citonga: Namwala Chibunze; Maseke S-02; Nanga S-03; Makunkha S-04