LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 9/14 tsa. 4
  • Zilengezo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zilengezo
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
km 9/14 tsa. 4

Zilengezo

◼ September ndi October: Gaŵilani magazini a Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani! November ndi December: Gaŵilani buku lamutu wakuti Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni kapena gaŵilani kalikonse ka tumapepala twa uthenga utu: Kodi Baibo Mumaiona Bwanji?, Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?, Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?, Kodi Ndani Maka-maka Amene Akulamulila Dzikoli?, Kodi Mavuto Adzathadi?, ndi kakuti Kodi N’zoona Kuti Akufa Angakhalenso ndi Moyo?

◼ Nkhani yapadela pambuyo pa Cikumbutso ca 2015 idzakambidwa mlungu wa April 6. Mutu wa nkhani imeneyi tidzauzidwa mtsogolo. Mipingo imene idzakhala ndi woyang’anila wadela kapena msonkhano wadela mlungu umenewo idzakhala ndi nkhaniyi mlungu wotsatila. Palibe mpingo umene uyenela kukhala ndi nkhani imeneyi mlungu wa April 6 usanafike.

◼ Kuyambila mwezi wa September, woyang’anila dela andzayamba kukamba nkhani ya anthu onse ya mutu wakuti “Kodi Nzelu Yocokela kwa Mulungu Imatipindulitsa Bwanji?”

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani