Zilengezo
◼ January ndi February: Gaŵilani kabuku kakuti, Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu. March ndi April: Gaŵilani magazini a Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani!
◼ Mutu wa nkhani ya onse ya woyang’anila dela pa ulendo waciŵili mu caka cautumiki ca 2015, udzakhala wakuti: “Zocitika za Padzikoli Zikusintha.”