Zilengezo
◼ Zogaŵila mu July ndi August: Uthenga Wabwino Wocokela Kwa Mulungu. September ndi October: Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani.
◼ Limbikitsani mabanja kuti abwelelemo mu zikumbutso za msonkhano wa cigawo zimene zili mu Utumiki Wathu wa Ufumu wa June 2015.