LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 June tsa. 2
  • June 6-12

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 6-12
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 June tsa. 2

June 6-12

MASALIMO 34-37

  • Nyimbo 95 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Khulupilila Yehova Ndipo Cita Zabwino”: (Mph. 10)

    • Sal. 37:1, 2—Ikani maganizo anu pa kutumikila Yehova, m’malo moganizila anthu oipa amene aoneka ngati zinthu ziwayendela bwino (w03 12/1 9-10 ndime 3-6 CN)

    • Sal. 37:3-6—Khulupililani Yehova, citani zabwino, ndipo mudzadalitsidwa (w03 12/1 10-12 ndime 7-15 CN)

    • Sal. 37:7-11—Yembekezelani Yehova moleza mtima mpaka ataononga anthu oipa (w03 12/1 13 ndime 16- 20 CN)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Sal. 34:18—Kodi Yehova amathandiza bwanji anthu a “mtima wosweka” ndi “odzimvela cisoni mumtima mwao”? (w11 6/1 19 CN)

    • Sal. 34:20—Kodi ulosi umenewu unakwanilitsidwa bwanji pa Yesu? (w13 12/15 21 ndime 19 CN)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Salimo 35:19–36:12

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani mavidiyo a maulaliki a citsanzo, ndipo kambilanani mfundo zake. Limbikitsani ofalitsa kukonza ulaliki wao.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 93

  • “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuseŵenzetsa Mavidiyo Pophunzitsa”: (Mph. 15) Kukambilana. Kuti mumvetsetse mfundo za pa kamutu kakuti “Mmene Tingacitile,” tambitsani vidiyo ya pa jw.org yakuti Ndani Analemba Baibulo? (Pitani polemba kuti MABUKU > MABUKU NDI TUMABUKU. Ndiyeno, pezani kabuku kakuti Uthenga Wabwino. Vidiyo imeneyi ipezeka pansi pankhani yakuti “Kodi Uthenga Wabwino Ni Wocokeladi kwa Mulungu?”)”)

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 17 ndime 1-13

  • Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 61 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani