LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsa. 4
  • July 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 July tsa. 4

July 11-17

MASALIMO 69–73

  • Nyimbo 92 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Anthu a Yehova ni Odzipeleka pa Kulambila Koona”: (Mph. 10)

    • Sal. 69:9—Kudzipeleka kwathu pa kulambila koona kuyenela kuonekela (w10 12/15-CN, masa. 7-11 ndime 2-17)

    • Sal. 71:17, 18—Acikulile angathandize acicepele kukhala odzipeleka (w14 1/1 , masa. 23-25 ndime 4-10)

    • Sal. 72:3, 12, 14, 16-19—Kudzipeleka kwathu kumatisonkhezela kuuzako ena zimene Ufumu wa Mulungu udzacitila anthu (w15 10/1 16 ndime 3; w10 8/15-CN, tsa. 32 ndime 19-20)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Sal. 69:4, 21—Kodi mavesi amenewa anakwanilitsika bwanji pa Mesiya? (w11 8/15-CN, tsa. 11 ndime 17; w11 8/15-CN, tsa. 15 ndime 15)

    • Sal. 73:24—Kodi Yehova amatsogolela bwanji anthu ake ku ulemelelo? (w13 2/15-CN, masa. 25-26 ndime 3-4)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 73:1-28

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Nsanja ya Mlonda ya 2016 Na. 4 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Nsanja ya Mlonda ya 2016 Na. 4 nkhani ya pacikuto

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) Uthenga Wabwino phunzilo 5 ndime 3-4

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 140

  • “Kodi Mungayeseko kwa Caka Cimodzi?”: (Mph. 15) Mwacidule, kambilanani nkhani imeneyi. Mukambilanenso “Ndandanda ya Upainiya wa Nthawi Zonse.” Onetsani ndi kukambilana vidiyo ya pa JW Broadcasting yakuti Khalani na Colinga Cimene Cidzakupindulitsani Kwamuyaya. (Pitani pa VIDEO ON DEMAND > TEENAGERS.)

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 19 ndime 17-31, bokosi pa tsa. 170, ndi kubwelelamo pa tsa. 171

  • Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 123 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani