LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 August tsa. 7
  • August 29–September 4

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 29–September 4
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 August tsa. 7

August 29–September 4

MASALIMO 110–118

  • Nyimbo 61 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Yehova Ndidzamubwezela Ciani?”: (Mph. 10)

    • Sal. 116:3, 4, 8—Yehova anapulumutsa wamasalimo ku imfa (w87 3/15-E, tsa. 24 ndime 5)

    • Sal. 116:12—Wamasalimo anafuna kuonetsa kuti amayamikila Yehova (w09 7/15-CN, tsa. 29 ndime 4-5; w98 12/1-CN, tsa. 24 ndime 3)

    • Sal. 116:13, 14, 17, 18—Wamasalimo anali wofunitsitsa kukwanilitsa udindo wake kwa Yehova (w10 4/15-CN, tsa. 27, bokosi)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Sal. 110:4—Kodi vesi imeneyi ikamba za lumbilo liti? (w14 10/15 tsa. 11 ndime 15-17; w06 9/1-CN, tsa. 14 ndime 1)

    • Sal. 116:15—Pokamba nkhani ya malilo, n’cifukwa ciani si bwino kugwilitsila nchito lemba la Salimo 116:15 pofotokoza za munthu womwalilayo? (w12 5/15-CN, tsa. 22 ndime 2)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 110:1–111:10

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya tsa. 16—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya tsa. 17—Yalani maziko a ulendo wina wobwelelako.

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) bh masa. 179-181 ndime 17-19—Thandizani wophunzila kuona mmene angaseŵenzetsele mfundo za m’nkhani imeneyo.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 82

  • “Phunzitsani Coonadi”: (Mph. 7) Kukambilana.

  • “Kampeni Yapadela Yogaŵila Nsanja ya Mlonda mu September”: (Mph. 8) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yoyamba ya citsanzo ca ulaliki mu September. Ndiyeno kambilanani zimene mwaphunzilapo. Limbikitsani ofalitsa kuti adzagwileko nchito yapadela imeneyi ndi kutengako upainiya wothandiza.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu  23 ndime 1-14

  • Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 144 na Pemphelo

    Cikumbutso: Lizani nyimbo yonse kamodzi, ndiyeno mpingo uyimbile pamodzi nyimboyo.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani