LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 January tsa. 6
  • January 23-29

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 23-29
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 January tsa. 6

January 23-29

YESAYA 38-42

  • Nyimbo 78 ena Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Yehova Amapeleka Mphamvu kwa Munthu Wotopa”: (10 min.)

    • Yes. 40:25, 26—Yehova ndiye Gwelo la mphamvu zonse (ip-1 409-410 pala. 23-25)

    • Yes. 40:27, 28—Yehova amaona mavuto na zinthu zopanda cilungamo zimene zimaticitikila (ip-1 413 pala. 27)

    • Yes. 40:29-31—Yehova amapeleka mphamvu kwa onse omudalila (ip-1 413-415 pala. 29-31)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yes. 38:17—Kodi Yehova amaponya bwanji macimo athu onse kumbuyo kwake? (w03 7/1 peji 17 pala. 17)

    • Yes. 42:3—Kodi ulosiwu unakwanilitsika bwanji pa Yesu? (w15 2/15 peji 8 pala. 13)

    • Kodi ine pacanga, kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ine pacanga ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. kapena zocepelapo) Yes. 40:6-17

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. kapena zocepelapo) fg—Kambilanani funso 1, pala. 1 m’phunzilo 8, ndipo yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 min. kapena zocepelapo) fg—Citani ulendo wobwelelako kwa munthu amene analandila kabuku ka Uthenga Wabwino mwa kupitiliza phunzilo 8.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. kapena zocepelapo) lv peji 38-39 pala. 6-7—Onetsani mmene tingam’fikile pamtima munthu.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 68

  • “Tizikumbukila Kupemphelela Akhiristu Anzathu Amene Akuzunziwa”: (15 min.) Kukambilana. Yambani mwa kutambitsa vidiyo yakuti Mlandu wa Mboni za Yehova Ulowanso mu Khoti ku Taganrog—Kodi Cilungamo Cidzacitika Liti? (Yendani ku mavidiyo pa GULU).

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 7 pala. 10-18, na kabokosi papeji 73

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 9 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani