LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 May tsa. 3
  • May 8-14

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 8-14
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 May tsa. 3

May 8-14

YEREMIYA 35-38

  • Nyimbo 33 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Ebedi-meleki—Citsanzo ca Kulimba Mtima na Kukoma Mtima”: (10 min.)

    • Yer. 38:4-6—Cifukwa coopa anthu, Zedekiya analola anthu otsutsa kuponya Yeremiya m’citsime ca matope (it-2 peji 1228 pala. 3)

    • Yer. 38:7-10—Pokhala wolimba mtima, Ebedi-meleki anathandiza Yeremiya (w12 5/1 peji 31 mapa. 2-3)

    • Yer. 38:11-13—Ebedi-meleki analinso wokoma mtima (w12 5/1 peji 31 pala. 4)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yer. 35:19—N’cifukwa ciani Arekabu anadalitsidwa? (it-2 peji 759)

    • Yer. 37:21—Kodi Yehova anam’samalila bwanji Yeremiya? Ndipo n’zotilimbikitsa bwanji tikakumana ndi zovuta? (w98 1/15 peji 18 mapa. 16-17; w95 8/1 peji 5 mapa. 5-6)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yer. 36:27–37:2

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) wp17.3 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) wp17.3 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wotsatila.

  • Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) jl phunzilo 26

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 127

  • “Kusamalila Malo Athu Olambilila” (15 min.) Mafunso na mayankho. Ikambidwe na mkulu. Pambuyo potambitsa vidiyo yakuti Kusamalila Malo athu Olambilila ndi kukambilana mafunso, mwacidule funsani mafunso ali pansipa m’bale wam’komiti yosamalila Nyumba ya Ufumu wa mumpingo mwanu. (Ngati mumpingo wanu mulibe m’baleyo funsani mgwilizanitsi wa bungwe la akulu.) Ngati mu Nyumba yanu ya Ufumu mumasonkhana mpingo wanu wokha, funsani woyang’anila zokonza-konza. Ni nchito ziti zokonza-konza pa Nyumba ya Ufumu zimene zacitika posacedwa, ndi zimene mufuna kudzacita kutsogoloku? Ngati wina ali na luso la zokonza-konza, kapena ngati afuna kuphunzila maluso mwa kuthandiza amene ali nawo kale, angacite bwanji? Kodi tonse, mosasamala kanthu za mmene zinthu zili pa umoyo wathu, tingathandizile bwanji kusamalila Nyumba ya Ufumu?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 12 mapa. 9-15, mabokosi papeji 122-123, ndi mapeji 130-131

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 125 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani