May 15-21
YEREMIYA 39-43
Nyimbo 133 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yehova Adzaweluza Aliyense Malinga na Nchito Zake”: (10 min.)
Yer. 39:4-7—Zedekiya anakumana ndi mavuto cifukwa cosamvela Yehova (it-2 peji 1228 pala. 4)
Yer. 39:15-18—Yehova anayamikila Ebedi-meleki cifukwa coonetsa cidalilo mwa Iye (w12 5/1 peji 31 pala. 5)
Yer. 40:1-6—Yehova anasamalila Yeremiya mtumiki wake wokhulupilika (it-2 peji 482)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yer. 42:1-3; 43:2, 4—Tiphunzilapo ciani pa zimene Yohanani analakwitsa? (w03 5/1 peji 10 pala. 10)
Yer. 43:6, 7—Kodi zocitika zochulidwa m’mavesiwa n’zofunika bwanji? (it-1 peji 463 pala. 4)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yer. 40:11–41:3
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) Yes. 46:10—Phunzitsani Coonadi. Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) Chiv. 12:7-9, 12—Phunzitsani Coonadi. Yalani maziko a ulendo wotsatila.
Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) bhs peji 160-161 pala. 19-20—Itanilani wophunzilayo kumisonkhano.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Yehova Saiŵala Cikondi Canu” (Sal. 71:18): (15 min.) Kukambilana. Yambani mwa kutambitsa vidiyo yakuti Yehova Saiŵala Cikondi Canu (mavidiyo MAPULOGILAMU NA ZOCITIKA ZINA).
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 12 mapa. 16-23, na mabokosi papeji 125 na 128; komanso bokosi lobwelelamo papeji 129
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 123 na Pemphelo