LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 June tsa. 4
  • June 12-18

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 12-18
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 June tsa. 4

June 12-18

MALIRO 1-5

  • Nyimbo 128 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Kuyembekezela Moleza Mtima Kumatithandiza Kupilila”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo ya Mfundo Zokhudza Buku la Maliro.]

    • Maliro 3:20, 21, 24—Yeremiya anayembekezela moleza mtima ndipo anadalila Yehova (w12 6/1 peji 14 mapa. 3-4; w11 9/15 peji 8 pala. 8)

    • Maliro 3:26, 27—Kupilila mayeselo kudzatithandiza kulimbana na zovuta zamtsogolo (w07 6/1 peji 11 mapa. 4-5)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Maliro 2:17—N’ciani cimene Yehova “ananena” cimene cinakwanilitsika cokhudza Yerusalemu? (w07 6/1 peji 9 pala. 4)

    • Maliro 5:7—Kodi Yehova amaimba anthu mlandu cifukwa ca zolakwa za makolo awo akale? (w07 6/1 peji 11 pala. 1)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Maliro 2:20–3:12

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) g17.3 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) g17.3 nkhani ya pacikuto—Itanilani mwininyumba kumisonkhano.

  • Nkhani: (6 mineti kapena kucepelapo) w11 9/15 9-10 ¶11-13—Mutu Wake: Yehova Ndi Colowa Canga.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 126

  • Zofunikila za Mpingo: (8 min.) Apo ayi, kambilanani “Kalata Yocokela ku Bungwe Lolamulila” mu Buku Lapacaka. (yb17 peji 2-5)

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya June 2017.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 13 mapa. 33-34, na bokosi “Zipambano za Kukhoti Zimene Zinapititsa Patsogolo Nchito Yolalikila, ndi bokosi lobwelelamo “Kodi Mumaona Kuti Ufumu wa Mulungu ndi Weniweni?”

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 100 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani