June 19-25
Ezekieli 1-5
Nyimbo 75 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Ezekieli Anasangalala Polengeza Uthenga wa Mulungu”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo ya Mfundo Zokhudza Buku la Ezekieli.]
Ezek. 2:9–3:2—Ezekieli anadya ‘mpukutu wa nyimbo zoimba polila, mau odandaula ndi olila’ (w08 7/15 peji 8 mapa. 6-7; it-1 peji 1214)
Ezek. 3:3—Ezekieli anali wosangalala kutumikila monga mneneli wa Yehova (w07 7/1 peji 12 pala. 3)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Ezek. 1:20, 21, 26-28—Kodi galeta lakumwamba limaimila ciani? (w07 7/1 peji 11 pala. 6)
Ezek. 4:1-7—Kodi Ezekieli anacitadi zinthu zofanizila kuzingidwa kwa Yerusalemu? (w07 7/1 peji 12 pala. 4)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Ezek. 1:1-14
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) T-32—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) T-32—Malizani mwa kum’tambitsa kavidiyo kakuti N’zotheka Banja Lanu Kukhala Lacimwemwe—Mau woyamba. Ndiyeno m’gaŵileni kabuku.
Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) bhs peji 151 mapa. 17—Onetsani mmene mungam’fikile pamtima wophunzila.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Muzisangalala Polalikila Uthenga Wabwino”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Pezaninso Cimwemwe mwa Kuphunzila na Kusinkha-sinkha.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 14 mapa. 1-7
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 32 na Pemphelo