LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 June tsa. 6
  • June 26–July 2

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 26–July 2
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 June tsa. 6

June 26–July 2

EZEKIELI 6-10

  • Nyimbo 141 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Kodi Mudzaikidwa Cizindikilo Kuti Mudzapulumuke?”: (10 min.)

    • Ezek. 9:1, 2—Masomphenya a Ezekieli akutiphunzitsa mfundo zothandiza (w16.06 peji 31-32)

    • Ezek. 9:3, 4—Amene amalandila uthenga umene timalalikila adzaikiwa cizindikilo kuti adzapulumuke mkati mwa cisautso cacikulu

    • Ezek. 9:5-7—Yehova sadzaononga anthu olungama pamodzi na oipa

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Ezek. 7:19—Kodi vesili likutithandiza bwanji kukonzekela zamtsogolo? (w09 9/15 peji 23 pala. 10)

    • Ezek. 8:12—Kodi vesili lionetsa bwanji kuti kusoŵa cikhulupililo kungacititse munthu kucita chimo? (w11 4/15 peji 26 pala. 14

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Ezek. 8:1-12

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) Chiv. 4:11—Phunzitsani Coonadi.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) Sal. 11:5; 2 Akor. 7:1—Phunzitsani Coonadi.

  • Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) bh 127 mapa. 4-5—Onetsani mmene mungam’fikile pamtima wophunzila.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 64

  • “Muzitsatila Miyezo ya Yehova ya Makhalidwe Abwino”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Khala Bwenzi la Yehova—Mwamuna M’modzi, Mkazi M’modzi

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 14 mapa. 8-14, na bokosi “Anafa Cifukwa Copeleka Ulemelelo kwa Mulungu”

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 33 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani