November 13-19
OBADIYA 1–YONA 4
Nyimbo 102 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Tizitengelapo Phunzilo pa Zolakwa Zathu”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Obadiya.]
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Yona.]
Yona 3:1-3—Yona anaphunzilapo kanthu pa zolakwa zake (ia peji 114 mapa. 22-23)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Obad. 10—Kodi Edomu ‘anawonongedwa mpaka kalekale’ motani? (w07 11/1 peji 13 pala. 5)
Obad. 12—Kodi tingaphunzilepo ciani pa cidzudzulo cimene Mulungu anapeleka kwa Aedomu? (jd peji 112 pala. 4-5)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yona 3:1-10
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) wp17.6 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) wp17.6—Onetsani ulendo wobwelelako mwa kuseŵenzetsa magazini imene inagaŵilidwa pa ulendo woyamba. Kenako, gaŵilani imodzi ya mabuku amene timatsogozela maphunzilo a Baibo.
Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) ld peji 12-13 (Sankhani mapikica amene mungakambilane.)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Zimene Tiphunzilamo m’Buku la Yona”: (15 min.) Kambilanani nkhaniyi pambuyo potamba vidiyo yakuti Kulambila kwa Pabanja: Yona Anaphunizilapo Kanthu pa Cifundo ca Yehova.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 21 mapa. 8-14
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 150 na Pemphelo