LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 December tsa. 3
  • December 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 December tsa. 3

December 11-17

ZEKARIYA 1-8

  • Nyimbo 26 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Adzagwila Covala ca Munthu Amene ndi Myuda”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Zekariya.]

    • Zek. 8:20-22—Anthu amitundu yonse akufuna-funa Yehova (w14 11/15 peji 27 pala. 14)

    • Zek. 8:23—Aja ali na ciyembekezo codzakhala padziko lapansi, amacilikiza otsalila odzozedwa mofunitsitsa (w16.01 peji 21 pala. 4; w09 2/15 peji 27 pala. 14)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Zek. 5:6-11—Kodi tili na udindo wanji tikadziŵa za coipa? (w17.10 peji 25 pala. 18)

    • Zek. 6:1—Kodi mapili aŵili amkuwa aimila ciani? (w17.10 mape. 27-28 mapa. 7-8)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Zek. 8:14-23

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) g17.6 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) g17.6 Onetsani ulendo wobwelelako mwa kuseŵenzetsa magazini imene inagaŵilidwa pa ulendo woyamba. Kenako, yalani maziko a ulendo wotsatila.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg Phunzilo 5 mapa. 1-2.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 70

  • “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kufikila Munthu Aliyense m’Gawo Lathu”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kulalikila “Mpaka Kumalekezelo a Dziko Lapansi”

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 22 mapa. 17-24, na bokosi lobwelelamo Kodi Mumaona Kuti Ufumu wa Mulungu ndi Weniweni?”

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 139 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani