December 18-24
ZEKARIYA 9-14
Nyimbo 8 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Khalanibe m’Cigwa ca ‘Pakati pa Mapili’”: (10 min.)
Zek. 14:3, 4—“Cigwa cacikulu kwambili” ciimila citetezo ca Mulungu (w13 2/15 peji 19 pala. 10)
Zek. 14:5—Amene ‘amathaŵila kucigwa’ na kukhala kumeneko adzatetezedwa (w13 2/15 peji 20 pala. 13)
Zek. 14:6, 7, 12, 15—Amene ali kunja kwa cigwa ca Yehova kapena kuti citetezo cake, adzawonongedwa (w13 2/15 peji 20 pala. 15)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Zek. 12:3—Kodi Yehova wasandutsa bwanji ‘Yerusalemu mwala wotopetsa’? (w07 12/15 mape. 22-23 mapa. 9-10)
Zek. 12:7—N’cifukwa ciani “coyamba Yehova adzapulumutsa mahema a Yuda”? (w07 12/15 peji. 25 pala. 13
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Zek. 12:1-14
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) g17.6 mapeji 14-15—Itanilani munthuyo ku misonkhano.
Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) g17.6 —Pa ulendo wapita, munakambilana mapeji 14 na 15 a magaziniyo. Citani ulendo wobwelelako na kuitanila munthuyo ku misonkhano.
Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) jl phunzilo 5—Itanilani munthuyo ku misonkhano.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo ya mwezi wa December yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa.
“Mbali Yatsopano pa Msonkhano wa Mkati mwa Wiki”: (8 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yopanda mau yakuti Betefage, Phili la Maolivi, na Yerusalemu.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy peji 6-7
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 13 na Pemphelo